Artist: → SevenOmore
{Pre-Chorus}
Ey-yoh, I’m high (I’m high)
I’m high (I’m high)
Somebody say, «I’m high» (I’m high)
{Chorus}
It’s a black panther party
Black panther party
It’s a black panther party
Black panther party
It’s a black panther party
Black panther party
It’s a black panther party
Black panther party
{Verse 1}
Down on my knees
Kumpempha Mlungu
Ambuye chonde ngwileni nkono
Nkhondo ndayiyambayi
Pandekha sindingathe
Kuli Angelo, anzake a satana
Akundinong’oneza, akundisokoneza
Andionetsa dziko
Ati landikulira
Ati nchifukwa chake ine ndiwobalalika
Ati nchifukwa chake zinthu zimatikanika
Koma nkati tachoka, tachoka, tachoka
Kamabwera kenanso, tachoka
Kubwera ka ulesi, tachoka
Kubweranso ka mantha, tachoka
Oh my God
{?}
DJ ta mixer ya Gina ilipati?
{Pre-Chorus}
Ey-yoh
I’m high
I’m high
I’m high
{Chorus}
It’s a black panther party
Party, party
It’s a black panther party
Party, party
It’s a black panther party
Party, party
It’s a black panther party
Party, party
{Verse 2}
Nakafikako tingoti ndinakachezako
Ku babiloniko nakagonako
Tingoti tinakawonako
Malamulo aja anangowasitha
{?}
There’s a land far, far away
It’s called Addis Ababa